Cart

 

Maphunziro a sayansi yamlengalenga paintaneti ndi mndandanda wa masatifiketi

Tsamba la EgSA la ukadaulo wa zamengalenga limapereka maphunziro ophunzirira pa intaneti ndi satifiketi aukadaulo pa sayansi ya zamlengalenga ndi ukadaulo wake. Maphunzirowa amapangidwa kuzela pa makanema ojambulidwa. Tsambalo limakhazikitsidwa ndikuyang'aniridwa ndi bungwe loyang’ana zamlengalenga laku Egypt (EgSA) kuti ipereke maphunziro aukadaulo okhuza ma satellite satalayiti, magawo a satalayiti, gawo la danga, gawo lapansi ndi ena.

Maphunzirowa amayamba kuchokera pamlingo woyambira ndipo amasunthira pang'onopang'ono kufikira akatswiri. Maphunziro, mayeso, ndi ziphaso zonse zimaperekedwa pa intaneti kudzera m'magawo atatu otsatirawa a maphunziro ndi zikalata:

  • Woyang'anira sayansi ya zamlengalenga ndi ukadaulo
  • Katswiri wa zamlengalenga ndi ukadaulo
  • Katswiri wogwira ntchito yoyang'anira ndi kulondoloza zamlengalenga

Maphunzirowa amafotokoza mitu yonse ya sayansi yamlengalenga komanso luso laukadaulo. Ophunzitsa athu ndi ovomerezeka komanso opanga maphunziro athu ndi oyenerera kwambiri, popeza akugwira ntchito yopanga ma satalayiti. Zomwe akumana nazo zimapangitsa kuphunzitsa kukhala kofunika komanso kosangalatsa.
Lembetsani Tsopano kuti mukhale ovomerezeka, kapena mutitumizire ife kuti mudziwe zambiri pa: info.portal@egsa.gov.eg

Maulalo ofunika: Tsamba lofikiraMitengoMwayi wolipililidwa maphunziroTumabukuLumikizanani nafe
 

Mndandanda wamaphunziro (The courses are available in English language only)

Woyang'anira sayansi ya zamlengalenga ndi ukadaulo

1 Kuyamba kwa maphunzilo akudaulo makonzedwe ndi kapitidwe ka satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
2 Kuyamba kwa Space Environment & Zotsatira zake pa Satellite Systems ophunzirira pa intaneti Zambiri
3 Kuyamba kwa maphunziro a ukadaulo wa sisitimu ya satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
4 Kuyamba kwa maphunziro a umekaniki wazozungulila ophunzirira pa intaneti Zambiri
5 Kuyamba kwa maphunziro ama sisitimu ang’onoang’ono a satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
6 Kuyamba kwa kusonkhanitsa, kuphatikiza, ndi kuyesa kwa satalayiti maphunziro ophunzirira pa intaneti Zambiri
7 Maphunziro a ntchito zoyanganila ndikukonzekela ntchito zamlengalenga ophunzirira pa intaneti Zambiri

Katswiri wa zamlengalenga ndi ukadaulo

8 Maphunziro a kapangidwe ka satalayiti ndi kalumikizidwe ka zipangizo zake ophunzirira pa intaneti Zambiri
9 Maphunziro a njira yoyendetsera kutentha kwa satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
10 Maphunziro a njira yamagetsi amu satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
11 Maphunziro a ndondomeko ya kayendedwe ka satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
12 Maphunziro akaziwidwe mlingo womwe satalayiti ili ndi kulamulilidwe kake ophunzirira pa intaneti Zambiri
13 Maphunziro a kuyankhulana kwa Satelayiti, Kutsata njila ndi kapelekedwe ka lamulo ophunzirira pa intaneti Zambiri
14 Maphunziro a kompyuta yokhala mu satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
15 Using Artificial intelligence in space imaging systems and its applications Online Course. Zambiri

Katswiri wogwira ntchito yoyang'anira ndi kulondoloza zamlengalenga

16 Kulandila nthaka Zambiri
17 Maphunziro a malo oyang'anira kawulukidwe ka satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri
18 Maphunziro a kuyamba kwa malo oyang’anila ndi kulamulila satalayiti ophunzirira pa intaneti Zambiri

To Top